Samad loved animals. His dream was to spend a whole day in a forest and sleep in the treehouse. Follow Samad as he embarked on this adventure where he made wonderful friends and amazing discoveries. Going into a forest has never been so much fun.
Samad anali okonda zinyama. Chokhumba cha moyo wake chinali kudzakhala tsiku lathunthu mu nkhalango ndi kugona mu nyumba ya mu mtengo. Mutsatileni Samad mmene akuyamba ulendo wake opita ku nkhalango komwe anakapanga maubwenzi ochititsa chidwi ndipo anakaona zinthu zodabwitsa zambiri. Kupita ku nkhalango ndi chinthu chosangalatsa kuposa china chilichonse.
Beli ebook ini dan dapatkan 1 lagi PERCUMA!
Format EPUB ● Halaman-halaman 26 ● ISBN 9781915637819 ● Saiz fail 5.8 MB ● Umur 17-10 tahun ● Penerbit Salaam Publishing ● Diterbitkan 2023 ● Edisi 1 ● Muat turun 24 bulan ● Mata wang EUR ● ID 9154693 ● Salin perlindungan Adobe DRM
Memerlukan pembaca ebook yang mampu DRM